chinyanja done

1




1

Werengani dongosolo la macitidwe a mayeso awa mwatsatane-tsatane ndi mosamala. 2 Musatsekule tsamba iri musanauzidwe kucita tero. Aphunzitsi anu adzakuuzani nthawi yotsekulira pepalali kuti muyambe kuyankha mafunso. 3 Pepala iri liri ndi mafunso okwanira makumi asanu (50) cabe mu zigawo zisanu ndi cimodzi. Muyankhe mafunso onse. Mukatsiriza kuyankha mafunso a m’cigawo cimodzi, musayembekezere kuuzidwa kuti mupite ku cigawo cina. Pitirizani kulemba mpaka kutsiriza mafunso onse. 4 Funso lirilonse liri ndi mayankho anai (4) amene limodzi cabe ndilo loyenera lopambana ena onse. Mukasankha yankho lanu, phimbani yankho lanulo pophimba mkombero muli yankho mwasankha motere. Yankho lacitatu ‘C’ ndilo lopambana onse. Conco phimbani yankho liri mu mkombero ‘C’. Werengani malangizo ndi zitsanzo zonse ziri m’cigawo ciriconse molingalira bwino ndiponso mosamala. Musanaphimbe yankho lanu muwerenge mayankho onse mosamala. 5 Ngati mufuna kusintha yankho mwasankha poyamba, fafanizani yankho loyamba mwaukhondo pogwiritsa nchito cofafanizira copanda dothi. 6 7 8 Musataye nthawi yaitali kufuna kuyankha mafunso olimba. Mungabwerere ku mafunsowo potsirizira pake ngati kwakhalako nthawi. Ngati mwatsiriza kuyankha mafunso onse, kukatsalako nthawi, gwiritsani nchito mphindi zotsalirazo kupititsamo mu mayankho anu. Onani kuti mwayankha mafunso onse. Imikani manja anu tsopano nciati: (i) Muli ndi funso. (ii) Pepalalanu la mayankho siliri lolongosoka. 1|Page

1

CIGAWO COYAMBA

Malangizo Funso lirilonse liyamba ndi ciganizo comwe ciri ndi liu kapena dera lina losowa m’malo amene aonetsedwa. Munsi mwake mudzapezamo mau kapena madera a ziganizo anai. Liu limodzi mwa mau anai ndilo lisiriza bwino ciganizo conse. Cisanzo: Myamata aliyense ali ndi kakhasu …….. kobzalira mtedza. A B C D kanga langa kake yake Yankho “C” kake, ndilo liu lisiriza bwino ciganizo conse. Conse munakaphimba yanho “C” mu mkomero motere: Tsopano yankhani mafunso otsatira: 1 Pa msonkhano wa azimai wacirezi kunabwera anthu ………. A acepa B kocepa C ocepa D tocepa 2 Dzina …….. ndine Malita, nanga iwe ndiwe ndani? A lake B lathu C langa D lanu 2|Page

CIGAWO COYAMBA

3 …….. dzina lake ndi Chimangeni Daka.

A Ine B Inu C Uyu D Iwo 4 Ine sindidzabwera kumsonkhano ………. Ndadwala malungo. A cifukwa B kapena C mwina D olo 5 Mnkhwere ndi dzina lina la nyama ya mthengo yomwe imachedwanso kuti …………… A mphaka. B mwanabere. C kambuku. D nyani. 6 Afakabelo akondedwa ndi anthu onse pamudzi pake cifukwa anali wa ………………. A manyonzo. B mwano. C umbombo. D ulemu. 7 Nsapato yake …….. yakuda inang’ambika dzulo. A ija B lija C tuja D zija 8 Daliyase analephera kukhoza mayeso cifukwa anali ………… A waluntha. B wanzeru. C waulesi. D wocenjera. 3|Page

3 …….. dzina lake ndi Chimangeni Daka.

9 Dera la Magwero ……………….. ku Chipata.

A apezeka B lipezeka C imapezeka D kapezeka 10 Yeremiya ayenda ……….. cifukwa analasidwa kuphazi ndi minga. A mofulumira B monyada C motang’adza D mosimphina 11 …………….. wobiriwira unapha mbuzi. A Cilumbusha B Kasokolowe C Msipu D Nthudza 12 …………..! yandiluma pa diso cenjere. A Haaa B Inee C Mainee D Ooo 13 Atsikana a kumudzi …….. Galuwawo akonda kubvina cimtali. A ku B kwa C pa D wa 14 Kumsonkhano wa zaulimi kunabwera anthu ………… A wambiri B wocepa C yambiri D zambiri 4|Page

9 Dera la Magwero ……………….. ku Chipata.

15 Buku …….. liri pathebulo ndi langa.

A amene B cymene C imene D limene CIGAWO CACIWIRI Cigawo ici ndi mbali ziwiri. Mbali yoyamba iri ziganizo zimene ziri mucindunji ndi mcisandunji (direct and indirect speech) Mbali yaciwiri iri ndi mafunso pa zopumira. Yankhani mafunso kulingana ndi malangizo opezeka pambali iri yonse. A Cindunji ndi cisandunji (direct and indirect speech) sankhani ziganizo zimene zalembedwa moyenera mwaziganizo zopezeka pa amfunso 16 ndi 17. 16 A B C D Zamene anena anthu awa ndi zoona. Zimene anena anthu awa ndi zoon. Zimene banana banthu aba ndi zoona. Zimene wanena awa wanthu ndi zoona. 17 A B C D “Ndizakhoza mayeso anga,” anatero Zilose. Ndizakhoza mayeso anga”anatero Zilose” “Ndizakhoza mayeso anga, anatero Zilose” “Ndizakhoza mayeso anga anatero Zilose 5|Page

15 Buku …….. liri pathebulo ndi langa.

ZOPUMIRA

MALANGIZO Mbali ya funso lirilonse liri ndi ciganizo comwe sicinaikidwe zopumira. M’malo onse amene mufunika zopimira mwaikidwa manambala. Munsi mwa ciganizo ciriconse mudzapezamo njira yosonyera kaikidwe ka zopumira m’malo muli munambala muja Citsanzo kusukulu lero (1) taphunzira masamu ndi cinyanja cabe (2) Pamene takomboka (3) tinapita ku munda wa sukulu kukalima (4). 1 2 3 4 , , . . , . . ? , ! ? . . ? . . A B C D Yankho ‘A’ ndilo laikidwa zopumira muyenera. Conco munakaphimba yankho ‘A’ mu mkombero motere: Tsopano yankhani mafunso otsatira awa: 18 Kodi mukupita kuti (1) ndaona nonse mutuluka mkalasi (2) kodi ndipite nanu (3) cifukwa ndi nthawi yopumula tsopano (4). 1 A B C D 2 3 4 ? ? . . ? ? . ? , ? , ? , ? ? . 6|Page

ZOPUMIRA

19 Kodi mwana uyu alibe malaya ndi wa ndani(1)cifukwa ninji

musunga ana tere (2)pitani mukamubvalike(3)muzisamala ana anu bwino(4) 1 C D 3 4 . , . ? , ? ? ! B 2 ? , A ? . . . . ? 20 Patsiku lokumbukira ufulu wathu wodzilamulira(1)anthu ambiri amabvina(2)kumwa(3)kudya ndi kupembedza mulungu pa zomwe anawacitira(4) 4 1 2 3 A . , , . B ! . , , C , ! . . D , , , . CIGAWO CACITATU Malangizo M’cigawo ici, funso lirilonse liri ndi ziganizo zinai zimene ziri manambala osaikidwa mu mndandanda wabwino. Ikani ziganizo izi mu m’ndandanda wadongosolo labwino kuti zonenedwa zonse zikhale zomveka. 7|Page

19 Kodi mwana uyu alibe malaya ndi wa ndani(1)cifukwa ninji

Werengani ziganizo zonse mosamala ndi kusankha njira

yolongosoka motsatiramanambala kuti zikhale mudongosolo lomveka bwino. Citsanzo: 1 kodi ndiwe munthu wa mtundu wanji. 2 sitidzayenda nawenso kuyambira lero 3 wosafuna kudzisamalira? 4 umangoticititsa manyazi pagulu la atsikana Yankho “C” ndilo longosoka mumndandanda. Nkhani yonse iyenera kukhala tere. 1 kodi ndiwe munthu wa mtundu wanji. 3 wosafuna kudzisamalira? 4 umangoticititsa manyazi pagulu la atsikana 2 Sitidzaenda nawenso kuyambira lero. Tsopano yankhani mafunso awa: 21 Sankhani ciganizo colongosoka. A B C D 1 2 3 4 22 1 2 3 4 A B C D 8|Page Mukanabwera dzulo, mukanandipeza. Mukanabwera dzulo, mukanandipeza. Mukanabwera mailo, mukanandipeza. Mukanabwera zulo, mukanandipeza. Ndiponso ndi nyama yopanda mphamvu. Thupi lake ndi lalikulu ku mutu koma ndi locepa kumcira Miyendo yake yakutsogolo ndi yaitali yakumbuyo ndi yaifupi Fisi ndi nyama yodabwitsa m’maonekedwe ake. 3 4 1 3 1 1 2 4 2 3 4 1 4 2 3 3

Werengani ziganizo zonse mosamala ndi kusankha njira

23 1

2 3 4 A B C D umabisa zakudya zako bwanawe ndiwe wojenjera uyenera kusintha khalidwe lako zakho umadya wekha. 2 3 1 4 3 2 1 4 4 1 2 3 2 1 4 3 24 1 Pambuyo paphunziro limenelo, Yona anakweza dzanja lake nafunsa aphunzitsi akewo funso lakuti. Tsiku lina ana a Giledi 7 amaphunzira za mbiri yakale ya Zambia. “kodi a prezidenti woyamba a dziko la Zambia anali ndani?” Apunzitsi anayankha nati, anali a prezident Kennth David Kaunda. 2 3 4 2,1,3,4 25 Sankhani ciganizo coyenera cymene cingapangidwe ndi mau awa, cizimyalupsya yoyamba ndiyo mvula. A Ndiyo cizimyalupsya yoyamba mvula. B Cizimyalupsya ndiyo mvula yoyamba. C Mvula ya cizimyalupsya ndiyo yoyamba. D Yoyamba ndiyo cizimyalupsya ya mvula. CIGAWO CACINAI Malangizo Mcigawo ici mudzayesedwa ngati mungathe kudziwa matanthauzo a mau, madera aziganizo kapena ziganizo zomwe. Munsi mwafunso lirilonse muli mayankho anai. Yankho limodzi cabe ndilo lopambana ena onse. Phimbani yankho mwasankha monga mwasonyezedwa pansipa. Citsanzo: Tikati Belita wapsa mtima ndiko kuti ………… A anatentha mtima. 9|Page

23 1



Flipbook Gallery

Magazines Gallery

Catalogs Gallery

Reports Gallery

Flyers Gallery

Portfolios Gallery

Art Gallery

Home


Fleepit Digital © 2021